Pologalamu ya Malonje imakhala ndi nyimbo zosiyana siyana za mu Africa komanso omvela amapeleka moni kwa okondwedwa awo.
Malonje (Chinyanja)
18 clip(s)
Ndakatulo yolira a Saulos Chilima ndi anthu ena asanu ndi atatu ku Malawi
Oyimba wa Ku Malawi Mr Thompo walimbikitsa oyimba a mdziko la South Africa
Oyimba wa ku Malawi Master Manda waonetsa kuti khama limapindula