President wa dziko la Malawi Lazarus Chakwera, wafika mdzikolo kuchokela ku dziko la United Arab Emirates komwe anakakambilana ndi mtsogoleri wa dzikolo Mohamed bin Zayed Al Nahyan zokuti boma lake lidzigulitsa mafuta ku boma la Malawi komanso zokuti makampani a dzikolo adzichita malonda mdziko la Malawi mwa zina.
Hastings Blessings Jumbe ali nkhani yonse.