Mtsogoleri wa dziko la Malawi Lazarus Chakwera walamula kuti ripoti yazotsatira za ngozi yomwe inapha wachiwiri kwa mtsogoleri wa dzikolo Dr Saulos Chilima ndi anthu ena asanu ndi atatu 8 liperekedwe ku ma banja onse okhudzidwa.
Mtolankhani wa Channel Africa mdziko la Malawi Kondwani Nyamasauka ali ndi nkhani yonse.