Zochitika (Chinyanja)Zochitika (Chinyanja)

President wa Malawi Lazarus Chakwera wabwelako ku ulendo wa ku UAE

View descriptionShare

President wa dziko la Malawi Lazarus Chakwera, wafika mdzikolo  kuchokela ku dziko la United Arab Emirates komwe anakakambilana ndi  mtsogoleri wa dzikolo Mohamed bin Zayed Al Nahyan zokuti boma lake lidzigulitsa mafuta ku boma la Malawi komanso zokuti makampani a dzikolo adzichita malonda mdziko la Malawi mwa zina.

Hastings Blessings Jumbe ali nkhani yonse.

 

  • Facebook
  • X (Twitter)
  • WhatsApp
  • Email
  • Download

In 1 playlist(s)

  1. Zochitika (Chinyanja)

    574 clip(s)

Zochitika (Chinyanja)

Current Affairs featuring various segments. 
Recent clips
Browse 714 clip(s)