President wa dziko la Botswana Mokgweetsi Masisi akucheza mdziko la Mozambique kufikila lachisanu sabata ino komwe akambilane zolimbitsa ubale pakati pa mayikowa.
Bright Sonjela akufotokoza
Zochitika (Chinyanja)
503 clip(s)
Chipani cha mlangizi wakale wa Renamo sichizachita masankho ku Mozambique
Anthu ena ku Zambia adzudzula president Hichilema posintha nduna ya za umoyo
Chiwelengelo cha anthu odzipha mdziko la Malawi chikuchulukila