Anthu okwana 51 a mdziko la Mozambique amene akukhala ku South Africa akusowa pokhala pamene nyumba zawo pomodzi ndi katundu zaotchedwa m’dela la Mamelodi mu mzinda wa Pretoria. Bright Sonjela akufotokoza nkhani yonse

Msonkhano wa zi ntchito za njanji wa Africa Rail wamalizika
06:14

Mabungwe ena ku Zambia ati a Hichilema asapange kampeni ndi katundu wa boma
08:44

Chionetselo cha za malonda cha Internationational Trade Fair chatha ku Zambia
06:54