Chionetselo cha za molonda cha International Trade Fair chafika lero kumapeto mdziko la Zambia komwe mayiko 23 anatenga nawo mbali pamodzi ndi nthumwi zoposa 1000. Ziyenela Zimba wadza ndi zambiri.

Msonkhano wa zi ntchito za njanji wa Africa Rail wamalizika
06:14

Mabungwe ena ku Zambia ati a Hichilema asapange kampeni ndi katundu wa boma
08:44

Aphungu atsegulira nyumba ya malamulo ku Malawi
07:24