Zochitika (Chinyanja)Zochitika (Chinyanja)

Mzika 51 za ku Mozambique zawotcheledwa nyumba ku South Africa

View descriptionShare
 

Anthu okwana 51 a mdziko la Mozambique amene akukhala ku South Africa akusowa pokhala pamene nyumba zawo pomodzi ndi katundu  zaotchedwa m’dela la Mamelodi mu mzinda wa Pretoria. Bright Sonjela akufotokoza nkhani yonse

  • Facebook
  • X (Twitter)
  • WhatsApp
  • Email
  • Download

In 1 playlist(s)

Zochitika (Chinyanja)

Current Affairs featuring various segments. 
Recent clips
Browse 1,029 clip(s)