Msonkhano wa zi ntchito za njanji wa Africa Rail wamalizika lero. Msonkhanowu, omwe unali wa masiku awiri, umachitikira pa malo otchedwa Sandton Convention Centre mzinda wa Johannesburg mchigawo cha Gauteng mdziko la South Africa ndipo cholinga chake chinali kufuna kukambirana mwa njira zina zomwe zingakhazikitsidwe pa kukweza zintchito zina mu gawoli. Thamo Kapisa anali komweko ndipo wabwela ndi zambili.

Mabungwe ena ku Zambia ati a Hichilema asapange kampeni ndi katundu wa boma
08:44

Chionetselo cha za malonda cha Internationational Trade Fair chatha ku Zambia
06:54

Aphungu atsegulira nyumba ya malamulo ku Malawi
07:24