President wa dziko la Mozambique Filipe Nyusi wati kafuku fuku pa kuphedwa kwa akulu akulu awiri a chipani chosutsa cha podemos amene anaphedwa loweluka sabata yatha ndi anthu osadziwika bwino. Matupi a kulu akuluwa ayikidwa m’manda lero ndipo a Nyusi ati mchitidwewu siwabwino . Iwo apempha anthu kuti adekhe asachitenso ziwonetselo. Mtolankhani mzathu mchigawo cha Niassa mdziko la Mozambique , Bright Sonjela akufotokoza