Zochitika (Chinyanja)Zochitika (Chinyanja)

Malawi akukondwelera zaka 62 za ufulu odzilamulira

View descriptionShare
 

Zochitika (Chinyanja)

Current Affairs featuring various segments. 
886 clip(s)
Loading playlist

Anthu a mdziko la Malawi ati dzikolo silikutukuka mu zinthu zambiri ngakhale likukondwelera kuti lakwanitsa zaka 62 chikhalireni pa ufulu odzilamulira kuyambila mchaka cha 1964. Jayne Chilamampunga wamva maganizo katswili olankhula pa nkhani zosiyana siyana mdzikolo a Imran Saidi

  • Facebook
  • X (Twitter)
  • WhatsApp
  • Email
  • Download

In 1 playlist(s)

Zochitika (Chinyanja)

Current Affairs featuring various segments. 
Recent clips
Browse 1,029 clip(s)