Zochitika (Chinyanja)Zochitika (Chinyanja)

Mabungwe oyang’anila masankho ati masankho anayenda mwabata ku Rwanda

View descriptionShare

Mabungwe oyang’anira masankho omwe antenga malo mdziko la Rwanda, lero atulutsa lipoti la momwe masankho mdzikoli ayendetsedwera. Nzika za dziko la Rwanda zinaponya mavoti pa 15 July osankha mtsogoleri ndi aphungu a nyumba ya malamulo. Mtsogoleri wapakali pano Paul Kagame amapikisana ndi Frank Habeneza wa chipani cha Green Democratic Party, ndi Phillipe Mpayimana oziyimira payekha. Ntola nkhani wa Channel Africa Micheal Mbewe wadza ndi nkhaniyi

  • Facebook
  • X (Twitter)
  • WhatsApp
  • Email
  • Download

In 1 playlist(s)

  1. Zochitika (Chinyanja)

    503 clip(s)

Zochitika (Chinyanja)

Current Affairs featuring various segments. 
Recent clips
Browse 640 clip(s)