Zochitika (Chinyanja)Zochitika (Chinyanja)

Mabungwe ena ku Malawi adzudzula zomwe Alexious Kamangila akulankhula

View descriptionShare
 

Zochitika (Chinyanja)

Current Affairs featuring various segments. 
821 clip(s)
Loading playlist

Mabungwe omenyela ma ufulu a anthu mdziko la Malawi a MABLEM  ndi HRCC adzudzula mchitidwe ogwilitsa ntchito masamba amchezo molakwikika  pamene loya  wina Alexious Kamangila akutchula akulu akulu ena kuti akuchita za katangale . Jayne Chilimampunga wabwela ndi nkhani yonse

  • Facebook
  • X (Twitter)
  • WhatsApp
  • Email
  • Download

In 1 playlist(s)

Zochitika (Chinyanja)

Current Affairs featuring various segments. 
Recent clips
Browse 964 clip(s)