Khothi la Machindye ku Kampala mdziko la Uganda, layimitsa kumva mlandu wa loya komanso mtsogoleri wa chipani cha People's Front for Freedom, Erias Lukwago, womwe ukumuneneza mlandu wofuna kulanda.Khothilo lati Lukwago sanathe kubwera kukhoti chifukwa akulandira chithandizo chapadera kuchipatala atadwala ali m'ndende. Mlanduwu uyambiranso pa 9 Julayi, pamene khothi lidzalandire lipoti la thanzi lake komanso momwe kafukufuku wa boma ukuyendera. Alfred Dzaoneni ali ndi zambiri

Msonkhano wa zi ntchito za njanji wa Africa Rail wamalizika
06:14

Mabungwe ena ku Zambia ati a Hichilema asapange kampeni ndi katundu wa boma
08:44

Chionetselo cha za malonda cha Internationational Trade Fair chatha ku Zambia
06:54