Bwalo lalikulu la za milandu mdziko la Zambia la Constitutional Court, lagamula kuti president wakale wa dzikolo Edgar Lungu asazapikisane pa masankho omwe adzachitike mchaka cha 2026 chifukwa chokuti analamula dzikolo kwa matelemu awiri malingana ndi malamulo a dzikolo.
Ziyenela Zimba wabwela ndi nkhaniyi.