Zochitika (Chinyanja)Zochitika (Chinyanja)

Dziko la Kenya lakwanitsa zaka 61 liri pa ufulu odzilamulira

View descriptionShare

Zochitika (Chinyanja)

Current Affairs featuring various segments. 
574 clip(s)
Loading playlist

Dziko la Kenya likukumbukira tsiku lomwe linalandira ufulu kuchoka mmanja mwa atsamunda aku Britain.Ndipo dzikoli lakwanitsa zaka 61 lili pa ufulu odzilamulira palokha.

A pulezidenti a dziko la Kenya anayankhula pamwambo wapadela okondwelera tsikuli lero  mu mzinda wa Nairobi.

Alfred Dzaoneni yemwe ndi mtolankhani nzathu kum’mawa kwa Africa akufotokoza zambiri.

 

  • Facebook
  • X (Twitter)
  • WhatsApp
  • Email
  • Download

In 1 playlist(s)

  1. Zochitika (Chinyanja)

    574 clip(s)

Zochitika (Chinyanja)

Current Affairs featuring various segments. 
Recent clips
Browse 714 clip(s)