Dziko la Kenya likukumbukira tsiku lomwe linalandira ufulu kuchoka mmanja mwa atsamunda aku Britain.Ndipo dzikoli lakwanitsa zaka 61 lili pa ufulu odzilamulira palokha.
A pulezidenti a dziko la Kenya anayankhula pamwambo wapadela okondwelera tsikuli lero mu mzinda wa Nairobi.
Alfred Dzaoneni yemwe ndi mtolankhani nzathu kum’mawa kwa Africa akufotokoza zambiri.