Zochitika (Chinyanja)Zochitika (Chinyanja)

Chipani cha UTM chatuluka mu Tonse Alliance mdziko la Malawi

View descriptionShare

Chipani cha United Transformation Movement -UTM  cha mdziko la Malawi chalengeza kuti tsopano chatuluka mumgwirizano omwe chinapanga  ndi chipani cha Malawi Congress Party -MCP  otchedwa Tonse Alliance. izitu zanenedwa pamsonkhano wa atolankhani lero mumzinda wa Lilongwe. Mtolankhani mzathu Kondwani Nyamasauka  anali nawo pa msonkhanowu ndipo akusimba

  • Facebook
  • X (Twitter)
  • WhatsApp
  • Email
  • Download

In 1 playlist(s)

  1. Zochitika (Chinyanja)

    503 clip(s)

Zochitika (Chinyanja)

Current Affairs featuring various segments. 
Recent clips
Browse 640 clip(s)