Chipani cholamula boma mdziko la Malawi cha Malawi Congress Party chadzudzula zomwe chinayankhula chipani chotsutsa boma cha Democratic Progressive Party---DPP lamulungu latha pa 15 December kuti anthu aku Blantyre azimenya wina aliyense yemwe azikamba za MCP mderali. Mtolankhani mzathu mdziko la Malawi Kondwani Nyamasauka ali ndi nkhani yonse.