Zochitika (Chinyanja)Zochitika (Chinyanja)

Banki ya Zambia ili ndi cholinga choletsa kugwilitsa ntchito ndalama za kunja

View descriptionShare

Banki yaikulu ya mdziko la Zambia ya Bank of Zambia ikukonza chiganizo chakuyimitsa kugwiritsa ntchito ndalama zaku maiko akunja mu ntchito zamalonda zomwe zimachitika mkati mwa dzikolo.

Bankiyi ili ndi maganizo akuti chiletso chimenechi chidzalimbitsa mphamvu za ndalama ya kwacha komanso maziko azachuma cha dzikolo.

Koma mkulu wa  Tour Guides Association wa nkhalango yaku South Luangwa National Park m’boma la Mambwe, Suzyo Zimba ,wati chiganizo chimenechi chidzapha ma business ambiri.

Nkhani yonse ili ndi Daniel Elisha Banda.

  • Facebook
  • X (Twitter)
  • WhatsApp
  • Email
  • Download

In 1 playlist(s)

  1. Zochitika (Chinyanja)

    503 clip(s)

Zochitika (Chinyanja)

Current Affairs featuring various segments. 
Recent clips
Browse 640 clip(s)