A phungu a nyumba ya malamulo mdziko la Malawi, ayamba zokambirana zawo lero za chi number 52. Uwutu ndi mkumano wa chitatu chisinthireni boma kupita m’manja mwa President Arthur Peter Mutharika. Kondwani Nyamasauka ali ndi nkhani yonse

Msonkhano wa zi ntchito za njanji wa Africa Rail wamalizika
06:14

Mabungwe ena ku Zambia ati a Hichilema asapange kampeni ndi katundu wa boma
08:44

Chionetselo cha za malonda cha Internationational Trade Fair chatha ku Zambia
06:54