Anthu oposa 100 anamwalira pa zionetselo zomwe zikuchitika mdziko la Mozambique ndipo zipatala zikudzadza ndi anthu ovulala pamene anthu ambiri akuyendabe m’misewu kufuna kuti zotsatila za masankho omwe anachitika pa 09 october chaka chino zisavomelezedwe.
Bright Sonjela akusimba.