Anthu a mu mzinda wa Harare mdziko la Zimbabwe ali odandaula ndi kufa kwa nyama za mtchile pa mbuyo pokumwa madzi okuda a poison ku Nyanja komwe kumachokela madzi okumwa a mu mzindawu ya Chiruwa.
John Kassim akulongosola zambiri
Zochitika (Chinyanja)
574 clip(s)
President wa Malawi wati ripoti la ngozi ya ndege ya a Chilima lipita kwa a banja
Khothi ku Uganda lati boma lipeleke chindapusa kwa anthu ozunzidwa ndi zigawenga
Chipani cha MCP ku Malawi chadzudzula DPP polankhula zodzetsa ziwawa