Zochitika (Chinyanja)Zochitika (Chinyanja)

Anthu a ulumali ku Mozambique ati boma lipange njila zoti azivota pa masankho

View descriptionShare

Zochitika (Chinyanja)

Current Affairs featuring various segments. 
503 clip(s)
Loading playlist

Anthu a ulumali mdziko la Mozambique apempha boma kuti lipange njila zoti anthuwa azikhala ndi mwayi okaponya voti pamene anthu amalephela kukavota chifukwa cha mavuto osiyana siyana.

Bright Sonjela akutambasula nkhaniyi

  • Facebook
  • X (Twitter)
  • WhatsApp
  • Email
  • Download

In 1 playlist(s)

  1. Zochitika (Chinyanja)

    503 clip(s)

Zochitika (Chinyanja)

Current Affairs featuring various segments. 
Recent clips
Browse 640 clip(s)