Anthu ochita za malonda ang’ono ang’ono mdziko la Zambia apempha boma kuti liwathandize ndi ngongole ya ndalama zochitila ma business awo . Ziyenela Zimba walankhula ndi m’modzi mwa anthu amene amachita malonda a mtunduwu bambo Adrian Banda.

Msonkhano wa zi ntchito za njanji wa Africa Rail wamalizika
06:14

Mabungwe ena ku Zambia ati a Hichilema asapange kampeni ndi katundu wa boma
08:44

Chionetselo cha za malonda cha Internationational Trade Fair chatha ku Zambia
06:54