A katswili a ndale mdziko la Malawi alankhulapo pa za kutuluka kwa Governor wakale wa bank ya reserve ya mdzikolo a Dalitso Kabambe atuluka mchipani chosutsa boma cha DPP pomwe ati achita izi chifukwa akufuna kupititsa patsogolo umoyo wawo wa ndale.
George Mhango wabwela ndi nkhani yonse