CHINYANJA: Nduna ya zokopa alendo ku dziko la Malawi Micheal Usi wati ntchito zokopa alendo mdzikolo zapita pansi kwambili chifukwa cha kubuka kwa mlili wa covid-19, dziko la Malawi linakhazikitsa mwezi wa September kuti ndi mwezi wantchito zokopa alendo.
ENGLISH: Malawi’s tourism minister Micheal Usi has said that tourism activities have been adversely affected by the Covid-19 pandemic. Malawi observes the month of September as tourism month.

MUUNI WA ZA LUSO LA MAKONO NDI DANIEL BANDA
08:53

BUNGWE LA UNITED PURPOSE KU MOZAMBIQUE LIKHAZIKITSA MALO OTUNGIRA MADZI A UKHONDO
05:56

NJOBVU ZAYAMBA KUSAMUTSIDWA KUCHOKA KU LIWONDE NATIONAL PARK KU MALAWI
04:49