Nkulu wa bungwe la aziphunzitsi la Basic Education Teachers Union of Zambia kuchigawo cha kummawa Simon Botha wati chingakhale chinthu chobweretsa nsangala ngati boma lingalembe ntchito aphunzitsi a zaka zokwana 45 zakubadwa kapena kupyola pangono, Malamulo a dziko la Zambia amaletsa boma kulemba anthu a zaka zimenezi ntchito. Daniel Elisha Banda, Zambia.

MUUNI WA ZA LUSO LA MAKONO NDI DANIEL BANDA
08:53

BUNGWE LA UNITED PURPOSE KU MOZAMBIQUE LIKHAZIKITSA MALO OTUNGIRA MADZI A UKHONDO
05:56

NJOBVU ZAYAMBA KUSAMUTSIDWA KUCHOKA KU LIWONDE NATIONAL PARK KU MALAWI
04:49