News in ChinyanjaNews in Chinyanja

NDEMANGA YA KATSWIRI PA ZA MALAMULO KU MALAWI PA NKHANI YA CHILIMA NDI CHAKWERA

View descriptionShare

Katswiri pa malamulo a dziko la Malawi garton Kanchedzera wathilira ndemanga potsatira mau a mtsogoleri wa dzikolo Lazarus Chakwera oyimitsa ntchito za wachiwiri wake Saulos Chilima yemwe pamodzi ndi anthu ena akukhudzikdwa ndi katangale ndi ziphuphu malingana ndi lipoti la bugwe lakafukufuku la ACB. Jayne Chilimampunga, Malawi.

  • Facebook
  • Twitter
  • WhatsApp
  • Email
  • Download

News in Chinyanja

A news and current affairs show produced live by the current affairs team.
Social links
Recent clips
Browse 2,102 clip(s)