Anthu mu dziko la Zambia apelenga ndemanga pa mawu omwe mtsogoleri wadzikolo Hakainde Hichilema, walankhula kuti nzika za dzikolo komanso mafumu, atenge nawo gawo pa mbali yokweza chitukuko cha dzikolo. Mtolankhani wathu Ziyenela Zimba walankhula ndi Headman Kalinde wa m’chigawo cha ku m’mawa kwa dzikolo pa nkhaniyi.

MUUNI WA ZA LUSO LA MAKONO NDI DANIEL BANDA
08:53

BUNGWE LA UNITED PURPOSE KU MOZAMBIQUE LIKHAZIKITSA MALO OTUNGIRA MADZI A UKHONDO
05:56

NJOBVU ZAYAMBA KUSAMUTSIDWA KUCHOKA KU LIWONDE NATIONAL PARK KU MALAWI
04:49