News in ChinyanjaNews in Chinyanja

MABUNGWE OTHANA NDI ZIPHUPHU KU ZAMBIA AYAMBA KUGWIRA NTCHITO MOCHILIMIKA

View descriptionShare

Civil society in Zambia raises concern on anti-corruption bodies

CHINYANJA:  Zipani za ndale ndi anthu mdziko la Zambia ati ali odabwa ndi mmene mabungwe othana ndi ziphuphu ndi katangale akugwilira ntchito zawo mochilimika pamene chipani cha UPND chatenga boma kusiyana ndi nthawi ya ulamulilo wa chipani cha PF

ENGLISH:  Civil society in Zambia is concerned with good performance of the anti-corruption bodies since United Party for National Development leader Hakainde Hichilema came into power.

  • Facebook
  • X (Twitter)
  • WhatsApp
  • Email
  • Download

News in Chinyanja

A news and current affairs show produced live by the current affairs team.
Social links
Recent clips
Browse 2,102 clip(s)