Ripoti lomaliza la ngozi ya ndege yomwe inapha wachiwiri kwa president Dr Saulos Chilima ndi anthu ena asanu ndi atatu 8 pa 10 June chaka chatha, latulutsidwa ndi Nthambi yochita kafuku fuku wa ngozi za ndege mdziko la Germany ya Germany Federal Bureau of Air craft accident investigations ya BFU.
George Mhango ali ndi nkhani yonse...

Mada Phiri kucheza ndikatswili oyimba wa mdziko la DRC Feed Paul RP amene amadziwika
13:05

Oyimba wa manganje wa ku Mozambique Ricabana wati amanyadila kuyimba za chimidzi
10:48

Gulu la akatswili opanga ndikusoka zovala zosiyana siyana la PSV Luxury, ladziko la Malawi koma amakhala mdziko la South Africa, kucheza ndi Mada Phiri ndikutiuza mmene anayambila ntchito yawo
23:48