Malonje (Chinyanja)Malonje (Chinyanja)

Polisi ya Zambia yagwira akuluakulu 11 azipani zotsutsa za mgwirizano wa Tonse

View descriptionShare
 

Malonje (Chinyanja)

Upbeat music, interviewing artists interactive; have weekly feature on community members giving back to their communities.
50 clip(s)
Loading playlist

Polisi ya dziko la Zambia yagwira akuluakulu  khumi ndi m’modzi 11 azipani zotsutsa za mgwirizano wa Tonse Alliance pambuyo pakupezeka ndi zida za nkhondo zoopsya. Mkulu wa zipanizi ndi a Brian Mundubile amene akutengako mbali ku masankho a President.

Pakati pa wogwidwawa pali mpongozi wa malemu Edgar Chagwa Lungu, a Patrick Mwansa. Mlembi wa cabinet ya boma.

A Patrick Kangwa ndi amene alengeza nkhaniyi ku mtundu wa Zambia. Daniel Elisha Banda ali ndi nkhani yonse.

  • Facebook
  • X (Twitter)
  • WhatsApp
  • Email
  • Download

In 1 playlist(s)

Malonje (Chinyanja)

Upbeat music, interviewing artists interactive; have weekly feature on community members giving back 
Recent clips
Browse 60 clip(s)