Malonje (Chinyanja)Malonje (Chinyanja)

Pali kugawikana pakati pa boma la Zambia ndi Tonse Alliance za maliro a aLungu

View descriptionShare

Malonje (Chinyanja)

Upbeat music, interviewing artists interactive; have weekly feature on community members giving back to their communities.
34 clip(s)
Loading playlist

Pali kugawikana maganizo pakati pa boma la zambia ndi mgwilizano wa zipani zosutsa boma wa Tonse Alliance za ku malo oli-li-ra maliro a prezidenti wakale wa Zambia Edgar Chagwa Lungu pamene boma la dzikolo layimitsa kuti thupi la malemu Lungu linyamuke kuchoka mdziko la South Africa kupita ku Zambia lero.  Ziyenela Zimba wabwela ndi tsatane tsatane wa nkhaniyi.

  • Facebook
  • X (Twitter)
  • WhatsApp
  • Email
  • Download

In 1 playlist(s)

Malonje (Chinyanja)

Upbeat music, interviewing artists interactive; have weekly feature on community members giving back 
Recent clips
Browse 44 clip(s)