Anthu okwana 51 a mdziko la Mozambique amene akukhala ku South Africa akusowa pokhala pamene nyumba zawo pomodzi ndi katundu zaotchedwa m’dela la Mamelodi mu mzinda wa Pretoria.
Bright Sonjela akufotokoza nkhani yonse.

Bungwe la MANEB ku Malawi latulutsa zotsatila za mayeso a standadi 8 ndi fomu 2
05:42

Polisi ya Zambia yagwira akuluakulu 11 azipani zotsutsa za mgwirizano wa Tonse
09:16

Mabungwe ku Zimbabwe adzudzula boma kuti likuwononga ufulu opanga zionetselo
05:06