Malonje (Chinyanja)Malonje (Chinyanja)

Mwambo okumbukila malemu Saulosi Chilima wachitika ku Malawi

View descriptionShare

Malonje (Chinyanja)

Upbeat music, interviewing artists interactive; have weekly feature on community members giving back to their communities.
34 clip(s)
Loading playlist

President wa dziko la Malawi Dr Lazarus Chakwera,anatsogolera a Malawi pa mwambo okumbukila malemu Saulos Chilima yemwe anali wachiwiri wawo ndipo  mwambowu unachitikira m’boma la Mzimba pamene akubanja nawo anali ndi mwambo ngati omwewu ku kumudzi kwa Chilima m’boma la ntcheu. Mtolankhani mzathu mdziko la  Malawi  Kondwani Nyamasauka ali ndi nkhani yonse.

  • Facebook
  • X (Twitter)
  • WhatsApp
  • Email
  • Download

In 1 playlist(s)

Malonje (Chinyanja)

Upbeat music, interviewing artists interactive; have weekly feature on community members giving back 
Recent clips
Browse 44 clip(s)