Mtsogoleri wa dziko la Zambia Hakainde Hichilema, wadzudzula ziwawa za ndale zomwe zikuchitika m'madela ena a mdzikolo komanso salora kuti anthu azinzuzidwa ndi kuchitidwa nkhanza chifukwa cha ndale ndipo yemwe apezeke akutelo, lamulo lizigwila ntchito pa iye.
Ziyenela Zimba wadza ndi zambiri...

Bungwe la MANEB ku Malawi latulutsa zotsatila za mayeso a standadi 8 ndi fomu 2
05:42

Polisi ya Zambia yagwira akuluakulu 11 azipani zotsutsa za mgwirizano wa Tonse
09:16

Mabungwe ku Zimbabwe adzudzula boma kuti likuwononga ufulu opanga zionetselo
05:06