Kucheza ndi katswili wazoimba imba mdziko la Malawi Waxy Kay, pamene anatiuza za ulendo wake wa kudziko la South Africa, komaso kuimba ku birthday ya mzake.

Oyimba wa mdziko la Mozambique BS Music wati oyimba asamayike maso pa ndalama
13:35

Mada Phiri kucheza ndikatswili oyimba wa mdziko la DRC Feed Paul RP amene amadziwika
13:05

Oyimba wa manganje wa ku Mozambique Ricabana wati amanyadila kuyimba za chimidzi
10:48