Dziko la Malawi likukumbukila nawo sabata yolimbikitsa amayi kuyamwitsa ana komanso mwa kathithi ndi cholinga chokuti ana azikula mwa thanzi pamene mayiko pa dziko lonse la pansi akukumbukila sabatayi.
Jayne Chilimampunga ali ndi zambiri za nkhaniy...

Bungwe la MANEB ku Malawi latulutsa zotsatila za mayeso a standadi 8 ndi fomu 2
05:42

Polisi ya Zambia yagwira akuluakulu 11 azipani zotsutsa za mgwirizano wa Tonse
09:16

Mabungwe ku Zimbabwe adzudzula boma kuti likuwononga ufulu opanga zionetselo
05:06