Malonje (Chinyanja)Malonje (Chinyanja)

A Suleman apempha kuti madraiva oledzela azigula ma polo omwe awononga ku Malawi

View descriptionShare
 

Malonje (Chinyanja)

Upbeat music, interviewing artists interactive; have weekly feature on community members giving back to their communities.
50 clip(s)
Loading playlist

Pamene ngozi komanso kuonongeka kwa katundu wa mu misewu ikulu ikulu kwafika poonjeza mdziko la Malawi, spikala wa nyumba yamalamulo mdzikolo wapempha aphungu kuti akhazikitse lamulo lokhwimitsa zilango kwa anthu omwe amayendetsa galimoto ataledzera  ndi kugwetsa mapolo amagetsi amunsewo azikonza okha zinthuzi.

Kondwani Nyamasauka wadza ndi zambiri mu report ili.

  • Facebook
  • X (Twitter)
  • WhatsApp
  • Email
  • Download

In 1 playlist(s)

Malonje (Chinyanja)

Upbeat music, interviewing artists interactive; have weekly feature on community members giving back 
Recent clips
Browse 60 clip(s)