Mzika zina za dziko la Zambia zomwe zikukhala mdziko la South Africa zati masankho omwe anachitika sabata yatha mdzikolo akukhudza tsogolo la mabanja awo, chuma cha dziko, komanso chiyembekezo cha moyo wabwino. Channel Africa yacheza ndi zina mwa nzikazi mu mzinda wa Johannesburg mdziko la South Africa, ndipo Alex Nkhuku ali ndi zambiri.

Anthu ena ku Malawi akufuna nthambi zina za boma zikhale zoyima pa zokha
05:30

Boma la Mozambique lakhwimitsa chitetezo cha mankhwala ndi makatemela
06:47

Linda Kasonde, Brebner Changala apeleka chikalata chotsutsa masankho a ku Zambia
06:32