Pulezidenti Hakainde Hichilema wayamikira anthu onse a ku Zambia, kuphatikizapo amene anamuvotera komanso amene sanamuvotere, potsindika kuti aliyense ali ndi ufulu wosankha mtsogoleri amene akumufuna.Malinga ndi zotsatira za masankho zomwe zalengezedwa ndi bungwe loyendetsa zisankho la ECZ,a Hichilema apeza mavoti oposa 2.97 million pamene a Brian Mundubile apeza mavoti oposa 1.86 miliyoni. Nkhani yonse ili ndi Daniel Elisha Banda.

Anthu ena ku Malawi akufuna nthambi zina za boma zikhale zoyima pa zokha
05:30

Boma la Mozambique lakhwimitsa chitetezo cha mankhwala ndi makatemela
06:47

Linda Kasonde, Brebner Changala apeleka chikalata chotsutsa masankho a ku Zambia
06:32