Zochitika (Chinyanja)Zochitika (Chinyanja)

Makhothi onse atsekedwa mdziko la Zambia

View descriptionShare
 

Zochitika (Chinyanja)

Current Affairs featuring various segments. 
928 clip(s)
Loading playlist

Makhothi onse m’dziko la Zambia atsekedwa ndipo akuyang’aniridwa ndi asilikali, pomwe lero pa 24 August 2026  ndi tsiku lomaliza loti mtsogoleri wa Tonse Pamodzi Alliance, Brian Mundubile, apereke patition kapena kalata yotsutsa zotsatira za chisankho cha pa 13 August 2026. Zimenezi zachititsa kuti mabungwe angapo omenyera ufulu wa anthu atsutse zomwe boma lachita, ponena kuti kutsekedwa kwa makhothi komanso kuyang’aniridwa kwawo ndi asilikali ndikupondereza maufulu a anthu. Mada Phiri wamva zambiri kuchokela kwa Daniel Elisha Banda mtolankhani wa Channel Africa mdziko la Zambia.
 

  • Facebook
  • X (Twitter)
  • WhatsApp
  • Email
  • Download

In 1 playlist(s)

Zochitika (Chinyanja)

Current Affairs featuring various segments. 
Recent clips
Browse 1,071 clip(s)