Loya komanso womenyera ufulu wa anthu, a Linda Kasonde, a Brebner Changala ndi bungwe la LCK Freedom Foundation, apereka petition kapeni kuti chikalata ku Constitutional Court mdziko la Zambia, kupempha khotili kuti lilamule kuti pakhale chisankho china cha President, ponena kuti chisankho cha pa 13 August 2026 sichinayende mwa chilungamo pamene chikonzekero chakulumbiritsa President Hakainde Hichilema pa 1 September 2026 chafika pa chimake. Daniel Elisha Banda akulongosola.

Anthu ena ku Malawi akufuna nthambi zina za boma zikhale zoyima pa zokha
05:30

Boma la Mozambique lakhwimitsa chitetezo cha mankhwala ndi makatemela
06:47

Akatswili pa nkhani ku Malawi akhumudwa ndi kubedwa kwa K700 miliyoni ku NOCMA
07:54