Zochitika (Chinyanja)Zochitika (Chinyanja)

Akatswiri a zamalamulo ku Uganda atsutsa zakutula pansi kwa maloya aKizza Besgye

View descriptionShare
 

Zochitika (Chinyanja)

Current Affairs featuring various segments. 
928 clip(s)
Loading playlist

Akatswiri a za malamulo ambiri ku Uganda atsutsana ndi zomwe zachitika ku bwalo lamilandu la likulu ku Uganda pomwe maloya oyimira mulandu nkhalakale pandale a Kizza Besigye ndi anzawo a Obed Lutale anena kuti asiya kuwayimira iwowa pa mulandu wawo.Awiriwa akuyankha mulandu ofuna kulanda boma ladziko la Uganda ku khothi lalikulu ku Kampala.Mtolankhani wa Channel Africa  ku m’mawa kwa Africa Alfred Dzaoneni ali ndi zambiri.

  • Facebook
  • X (Twitter)
  • WhatsApp
  • Email
  • Download

In 1 playlist(s)

Zochitika (Chinyanja)

Current Affairs featuring various segments. 
Recent clips
Browse 1,071 clip(s)