Steve Paskolo wa gulu la kwaya ya East Rand ku South Africa wacheza pa malonjeOyimba mu gulu la kwaya la East Rand la mdela la Boksburg, mu mzinda wa Johannesburg, Mdziko la South Africa, Steve Paskolo wacheza pa ndi Stella Longwe muwulutsi wa Malonje pomwe wanena zambiri za nyimbo yomwe kwayayi inayimba yokuti tizikondana.
Powonjezela a Paskolo ati kwayayi ndi yogwilizana ngakhale kuti muli anthu ambiri chifukwa chokuti onse amasogoza chauta.