Zochitika (Chinyanja)Zochitika (Chinyanja)

Khothi la AFCHR lakana kumva pempho la A Chanthunya omwe anapha chibwenzi 

View descriptionShare

Bwalo  la  za milandu la African Court on Human Rights and Peoples Rights ,lakana kumva pempho la misozi chanthunya okuti khothili lichotse chilango chomwe anapatsidwa kuti aphike ndende moyo wake onse chifukwa chokupha chibwenzi chake linda gasa mzika ya ku zimbabwe mchaka cha 2010.

A chanthunya anati boma la Malawi linawaphwanyila ufulu wawo panthawi yomwe anazengedwa mulandu wakupha chibwenzi chawo.

George Mhango ali ndi nkhani yonse 

  • Facebook
  • X (Twitter)
  • WhatsApp
  • Email
  • Download

In 1 playlist(s)

  1. Zochitika (Chinyanja)

    556 clip(s)

Zochitika (Chinyanja)

Current Affairs featuring various segments. 
Recent clips
Browse 695 clip(s)