Zochitika (Chinyanja)Zochitika (Chinyanja)

Gulu la anthu linatenga zikwanje kuletsa otsutsa kuchita zionetselo ku Malawi

View descriptionShare

Gulu la anthu linatenga zikwanje kuletsa  zipani zotsutsa boma kuchita zionetselo mu mzinda wa Lilongwe mdziko Malawi zokakamiza mkulu wa bungwe lowona za masankho la Malawi Electoral Commission kuti atule pansi udindo komanso kuti bungwe lopanga ziphatso za umzika la NRB silikuyendetsa bwino ntchito yake pamene ntchito ya kaundula wa voti ili mkati.

Jayne Chilimampunga ali ndi nkhani yonse.

  • Facebook
  • X (Twitter)
  • WhatsApp
  • Email
  • Download

In 1 playlist(s)

  1. Zochitika (Chinyanja)

    556 clip(s)

Zochitika (Chinyanja)

Current Affairs featuring various segments. 
Recent clips
Browse 695 clip(s)