Zochitika (Chinyanja)Zochitika (Chinyanja)

Boma la Zimbabwe lati makampani amigodi ayamba kupanga magetsi pa okha 

View descriptionShare

Boma la Zimbabwe lalengeza kuti makampani a migodi maka maka omwe amakumba mwala wa chrome  adzayamba kupanga magetsi pa okha kumapeto a chaka chino ndi cholinga chochepetsa vuto la magetsi  pamene makampani a migodi amatenga 25 percenti ya magetsi .

John Kassim akulongosola zambiri za nkhaniyi

  • Facebook
  • X (Twitter)
  • WhatsApp
  • Email
  • Download

In 1 playlist(s)

  1. Zochitika (Chinyanja)

    556 clip(s)

Zochitika (Chinyanja)

Current Affairs featuring various segments. 
Recent clips
Browse 695 clip(s)