Wachiwiri kwa mtsogoleri wa Malawi wakale Micheal Usi wati atha kugwira ndi DPP
Wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko la Malawi wakale Dr Micheal Usi, wapempha boma la Democratic Progressive Party kuti liwalole kugwira nawo ntchito pofuna kuthetsa vuto lakusowa kwa mafuta a galimoto lomwe lafika posautsa mdzikolo.
Mtolankhani mzathu mdzikolo Kondwani Nyamasauka ali ndi nkhani yonse.



